Yo Maps – So Mone [Feat. Tay Grin] Lyrics

Yo Maps – So Mone [Feat. Tay Grin] ( Lyrics ) Letra Yo Maps Yo Yo Maps – So Mone [Feat. Tay Grin] ( Lyrics )
Yeah eh Ati no permanent Permanent Safuna mwamuna permanent Permanent ati nifuna mwamuna wa chizungu Wama Benz na mansion. Ali na chuma na ka cv. Opunzila na ka class. Apa Muna kwatilana so chili bwa, nimvela munkala ku konboni. Naine mulungi Ani sunga. Nina kwatila na tubana. Nina mvela kuti vina sila. Mwamuna wako ni mambala. Sorry ohh, Sorry ooh, Aibo!!!! Eeh Eeh Eeh!! So umvela bwanji ukanitamba pa tv yako iwe. Una sanka mwamuna wa tv not na nzelu, Kuli ine Wenzo ona fwaka. Banitenga bena bo ziba. SoMone So-Mone, So-Mone, Eeh Ehhe Eeh. So umvela bwanji ukanitamba pa tv yako iwe. Una sanka mwamuna wa tv not na nzelu..Kuli ine Wenzo ona Moba. Banitenga bena bo ziba.

UPDATE

1 ContributorSo Mone Lyrics

[verse 2: Tay Grin]
N’akuwuuza, osa meka, ah
Dekha fatsa zidzatheka, ah
Unandisiya chabe wekha
Apa ufuna tibwelеrane
N’akuwuuza, osa meka, ah
Dekha fatsa zidzathеka, ah
Unandisiya chabe wekha
Apa ufuna tibwelerane

[bridge: Tay Grin]
So, chilibwa?
So, chilibwa?
Ndagula nyumba ku 43’
Aa neighbor anga, ndi azungu
Ndalama zanga, ndi za chizungu
So, chilibwa?
So, chilibwa?
Ndagula nyumba ku 43’
Aa neighbor anga, ndi azungu
Ndalama zanga, ndi za chizungu

[Chorus: Yo Maps]
Eeh, so, umvela bwangi ukanitamba pa TV yako iwe?
Una sanka mwamuna wa TV not na nzelu, ohh
Muli ine wenzo ona fwaka
Bani tenga bena bo ziba
So mone
So mone-ee
So, umvela bwangi ukanitamba pa tv yako iwe?
Una sanka mwamuna wa Benz not na nzelu, ohh
Muli ine wenzo ona moba
Bani tenga bena bo ziba
So mone
So mone-ee

[verse 3: Yo Maps]
Ati, hold on
Wamanga bwangi ma nyumba aya?
Baby, hold on
Mukazi wa muchosa kuti, owama uyo?
Ija Benz, nina gula
Mansion, nina manga
Naka CV, nina panga (ahh)

[bridge: Tay Grin]
So, chilibwa?
So, chilibwa?
Ndagula nyumba ku 43
Aa neighbor anga, ndi azungu
Ndalama zanga, ndi za chizungu
So, chilibwa?
So, chilibwa?
Ndagula nyumba ku 43
Aa neighbor anga, ndi azungu
Ndalama zanga, ndi za chizungu

[Chorus: Yo Maps]
So, umvela bwangi ukanitamba pa TV yako iwe?
Una sanka mwamuna wa TV not na nzelu, ohh
Muli ine wenzo ona fwaka
Bani tenga bena bo ziba
So mone
So mone-ee

Advertisement