Crispy Malawi – Zikuti Bwa? Lyrics

Crispy Malawi – Zikuti Bwa? Crispy Malawi Crispy Malawi – Zikuti Bwa? Lyrics
Intro
Ndangovala lipha man ndi ma socks
This is real life si mikozi
Ndiku chaser bag ndi mkazi modzi
Ndi mkazi modzi
Ndi mkazi modzi
Hee hee heeee

Chorus
Zikuti bwa?
Ndikudziwa ukufila vibe
Koma ta talker zikuti bwa?
Tandipatse plan fast fast zikuti bwa?
Ma gee ndi babe otifila zikuti bwa?
Verse
Kungodzuka monaz Kumu halla homie zikuti bwa?
Jah jah Ali mbali yathu wati dzutsaso
Umati bwa?
Kodi nthawi ili bwanj?
Ngati ili four twenty Kumu caller plug zikuti bwa?
Zikuti bwa?
Pano Ndine main artist ndachoka pa many more
Ndima friends ena zikuti bwa?
Don’t talk anymore
Ma ex sindingavunge text or kumenya call
Siza hater wish you well Bola tonse tili bho

Chorus
Zikuti bwa?
Ndikudziwa ukufila vibe
Koma ta talker zikuti bwa?
Tandipatse plan fast fast zikuti bwa
Ma gee ndi babe odzifila zikuti bwa
Hee hee heeee
Zikuti bwa?
Ndikudziwa ukufila vibe
Koma ta talker zikuti bwa?
Tandipatse plan fast fast zikuti bwa?
Ma gee ndi babe odzifila zikuti bwa?
Outro
Ndangovala lipha man ndi ma socks
This is real life si mikozi
Ndiku chaser bag ndi mkazi modzi
Ndi mkazi modzi
Ndi mkazi modzi
Ndangovala lipha man ndi ma socks
This is real life si mikozi
Ndiku chaser bag ndi mkazi modzi
Ndi mkazi modzi
Ndi mkazi modzi
Lyrics, Letras, Paroles, Deutsche, Letras, Testi,Тексты, Texty, Norske, Текстови, Versuri, Persian, Liricí, Lirik, Nederlandse, Tagalog